-
Health
Chizolowezi chopha bongo (Adikishoni)
Kodi Adikishoni ndi chiyani? Adikishoni ndi chizolowezi maganizo kapena thupi (kapena zonse ziwiri) chopha umunthu chomwe chimadza pakugwiritsa ntchito zinthu…
Read More »Download PDF -
Ndi zizolowezi ziti zomwe zafala ku Malawi kuno?
Pali mitundu yosiyanasiyana ya zizolowezi za Adikishoni m’Malawi mwa anthu amisinkhu yosiyanasiyana. Ngakhale kuti akafukufuku ambiri ayang’ana za vuto la…
Read More » -
Ndani ali pachiwopsezo?
Kuledzera mwa Adikishoni ndizovuta kumvetsa. Pali zinthu zambiri zomwe zitha kupangitsa kuti chiwonjezeko chazovuta zi zichitike. Mwachitsanzo, kusokonezeka kwa mowa…
Read More » -
Kodi mungapewe zizolowezi zoipa?
Ngakhale kuti palibe njira imodzi kapena njira yotsimikizirika yoletsera munthu kuti asakhale ndi khalidwe linalake kapena zinthu zina, pali zinthu…
Read More » -
N’chifukwa chiyani muyenera kuda nkhawa ndi zizolowezi zoipa?
Adikishoni monga kumwa mowa ndi kugwiritsira ntchito mankhwala osokoneza bongo kuli ndi kuthekera kwakukulu kwa zovuta zakuthupi ndi zamaganizo. Adikishoni…
Read More »